2 Ndipo Mose analembera maturukidwe ao monga mwa maulendo ao, monga mwa mau a Yehova; ndipo maulendo ao ndi awa monga mwa maturukidwe ao.
Werengani mutu wathunthu Numeri 33
Onani Numeri 33:2 nkhani