12 Ndipo midziyo ikukhalireni yakupulumuka wolipsa; kuti wakupha mnzace asafe, kufikira ataima pamaso pa msonkhano amweruze.
Werengani mutu wathunthu Numeri 35
Onani Numeri 35:12 nkhani