Numeri 35:15 BL92

15 Midzi isanu ndi umodzi imene ndiyo yopulumukirako ana a Israyeli, ndi mlendo, ndi wokhala pakati pao; kuti ali yense adamupha munthu osati dala athawireko.

Werengani mutu wathunthu Numeri 35

Onani Numeri 35:15 nkhani