17 Kapena akamkantha m'dzanja muli mwala, wakufetsa munthu, ndipo wafa, ndiye wakupha munthu; wakupha munthu nayenso amuphe ndithu.
Werengani mutu wathunthu Numeri 35
Onani Numeri 35:17 nkhani