Numeri 35:21 BL92

21 kapena kumpanda ndi dzanja lace momuda, kuti wafa, womkanthayo nayenso amuphe ndithu; ndiye wakupha munthu; wolipsa mwazi aphe wakupha munthuyo pomkumika.

Werengani mutu wathunthu Numeri 35

Onani Numeri 35:21 nkhani