Numeri 35:23 BL92

23 kapena kumponyera mwala wakufetsa munthu, osamuona, namgwetsera uwu, kuti wafa, koma sindiye mdani wace, kapena womfunira coipa;

Werengani mutu wathunthu Numeri 35

Onani Numeri 35:23 nkhani