Numeri 35:32 BL92

32 Musamalandira dipo lakuombola iye amene adathawira ku mudzi wace wopulumukirako, kuti abwerenso kukhala m'dziko, kufikira atafa wansembe.

Werengani mutu wathunthu Numeri 35

Onani Numeri 35:32 nkhani