Numeri 4:23 BL92

23 Uwawerenge kuyambira a zaka makumi atatu ndi mphambu, kufikira a zaka makumi asanu; onse akulowa kutumikira utumikiwo, kucita nchitoyi m'cihema cokomanako.

Werengani mutu wathunthu Numeri 4

Onani Numeri 4:23 nkhani