5 akati amuke a m'cigono, Aroni ndi ana ace amuna azilowa, natsitse nsaru yocinga, ndi kuphimba nayo likasa la mboni,
Werengani mutu wathunthu Numeri 4
Onani Numeri 4:5 nkhani