13 ndi munthu akagona naye, koma kumbisikira maso a mwamuna wace, ndikumng'unira; nadetsedwa mkaziyo, koma palibe mboni yomtsutsa, kapena sanamgwira alimkucita;
Werengani mutu wathunthu Numeri 5
Onani Numeri 5:13 nkhani