22 ndipo madzi awa akudzetsa temberero adzalowa m'matumbo mwako, nadzakutupitsa mbulu ndi kuondetsa m'cuuno mwako; ndipo mkaziyo aziti, Amen, Amen.
Werengani mutu wathunthu Numeri 5
Onani Numeri 5:22 nkhani