26 Wansembe atengekonso nsembe yaufa wodzala manja, cikumbutso cace, nacitenthe pa guwa la nsembe; ndipo atatero amwetse mkazi madziwo.
Werengani mutu wathunthu Numeri 5
Onani Numeri 5:26 nkhani