Numeri 5:30 BL92

30 kapena pamene mtima wansanje umgwira mwamuna, ndipo acitira mkazi wace nsanje; pamenepo aziika mkazi pamaso pa Yehova, ndipo wansembe amcitire cilamulo ici conse.

Werengani mutu wathunthu Numeri 5

Onani Numeri 5:30 nkhani