6 Nena ndi ana a Israyeli, ndi kuti, Mwamuna kapena mkazi akacita cimo liri lonse amacita anthu, kucita mosakhulupirika pa Yehova, nakaparamuladi;
Werengani mutu wathunthu Numeri 5
Onani Numeri 5:6 nkhani