Numeri 6:17 BL92

17 naphe nkhosa yamphongo yoyamika ya Yehova, pamodzi ndi mtanga wa mkate wopanda cotupitsa; wansembe akonzenso nsembe yace yaufa, ndi nsembe yace yothira.

Werengani mutu wathunthu Numeri 6

Onani Numeri 6:17 nkhani