3 azisala vinyo ndi kacasu; asamwe vinyo wosasa, kapena kacasu wosasa, kapena cakumwa conse ca mphesa, asamwe; asadye mphesa zaziwisi kapena zouma.
Werengani mutu wathunthu Numeri 6
Onani Numeri 6:3 nkhani