7 Asadzidetse ndi atate wace, kapena mai wace, mbale wace, kapena mlongo wace, akafa iwowa; popeza cowindira Mulungu wace ciri pamutu pace.
Werengani mutu wathunthu Numeri 6
Onani Numeri 6:7 nkhani