Numeri 7:53 BL92

53 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa za mphongo zisanu, atonde asanu, ana a nkhosa asanu a caka cimodzi; ndico copereka ca Elisama mwana wa Amihudi.

Werengani mutu wathunthu Numeri 7

Onani Numeri 7:53 nkhani