15 Ndipo tsiku loutsa kacisi mtambo unaphimba kacisi, ndiwo cihema cokomanako; ndipo madzulo padaoneka pakacisi ngati moto, kufikira m'mawa.
Werengani mutu wathunthu Numeri 9
Onani Numeri 9:15 nkhani