21 Koma mtambo ukakhala kuyambira madzulo kufikira m'mawa; pokwera mtambo m'mawa, ayenda ulendo; ngakhale msana ngakhale usiku, pokwera mtambo, ayenda ulendo.
Werengani mutu wathunthu Numeri 9
Onani Numeri 9:21 nkhani