53 Koma Alevi amange mahema ao pozungulira pa kacisi wa mboni, kuti mkwiyo ungagwere khamu la ana a Israyeli; ndipo Alevi azidikira kacisi wa mboni.
Werengani mutu wathunthu Numeri 1
Onani Numeri 1:53 nkhani