28 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni, mtumiki wa Mose kuyambira ubwana wace, anayankha nati, Mose, mfumu yanga, aletseni.
Werengani mutu wathunthu Numeri 11
Onani Numeri 11:28 nkhani