Numeri 11:29 BL92

29 Koma Mose anati kwa iye, Kodi ucita nsanje nao cifukwa ca ine? Mwenzi anthu onse a Yehova atakhala aneneri! mwenzi Yehova atawaikira mzimu wace!

Werengani mutu wathunthu Numeri 11

Onani Numeri 11:29 nkhani