30 Cifukwa cace unene nao, Pamene mukwezako zokometsetsa zace, zidzayesedwanso kwa Alevi ngati zipatso za padwale, ndi zipatso za mopondera mphesa,
Werengani mutu wathunthu Numeri 18
Onani Numeri 18:30 nkhani