31 Ndipo muzidye pamalo ponse, inu ndi a pabanja panu; popeza ndizo mphotho yanu mwa nchito yanu m'cihema cokomanako.
Werengani mutu wathunthu Numeri 18
Onani Numeri 18:31 nkhani