32 Ndipo simudzasenzapo ucimo, mutakwezako zokometsetsa zace; ndipo musamaipsa zinthu zopatulika za ana a Israyeli, kuti mungafe.
Werengani mutu wathunthu Numeri 18
Onani Numeri 18:32 nkhani