Numeri 19:5 BL92

5 Pamenepo atenthe ng'ombe yamsotiyo pamaso pace; atenthe cikopa cace ndi nyama yace, ndi mwazi wace, pamodzi ndi cipwidza cace.

Werengani mutu wathunthu Numeri 19

Onani Numeri 19:5 nkhani