6 Ndipo wansembe atenge mtengo wamkungudza, ndi hisope, ndi ubweya wofiira, naziponye pakati pa mota irikupsererapo ng'ombe yamsoti.
Werengani mutu wathunthu Numeri 19
Onani Numeri 19:6 nkhani