Numeri 2:18 BL92

18 Mbendera ya cigono ca Efraimu izikhala kumadzulo monga mwa makamu ao; ndipo kalonga wa ana a Efraimu ndiye Elisama mwana wa Amihudi.

Werengani mutu wathunthu Numeri 2

Onani Numeri 2:18 nkhani