17 Pamenepo khamu la Alevi azimuka naco cihema cokomanako, pakati pa makamu; monga amamanga mahema ao, momwemo azimuka ulendo wao, munthu yense pamalo pace, monga mwa mbendera zao.
Werengani mutu wathunthu Numeri 2
Onani Numeri 2:17 nkhani