3 Ndipo anthu anatsutsana ndi Mose, nanena, nati, Mwenzi titangomwalira muja abale athu anamwalira pamaso pa Yehova!
Werengani mutu wathunthu Numeri 20
Onani Numeri 20:3 nkhani