Numeri 24:7 BL92

7 Madzi adzayenda naturuka m'zotungira zace,Ndi mbeu zace zidzakhala ku madzi ambiri,Ndi mfumu yace idzamveka koposa Agagi,Ndi ufumu wace udzamveketsa.

Werengani mutu wathunthu Numeri 24

Onani Numeri 24:7 nkhani