8 Mulungu amturutsa m'Aigupto;Ali nayo mphamvu yonga ya njati;Adzawadya amitundu, ndiwo adani ace.Nadzaphwanya mafupa ao, Ndi kuwapyoza ndi mibvi yace.
Werengani mutu wathunthu Numeri 24
Onani Numeri 24:8 nkhani