9 Anaunthama, nagona pansi ngati mkango,Ngati mkango waukazi; adzamuutsa ndani?Wodalitsika ali yense wakudalitsa iwe,Wotemberereka ali yense wakutemberera iwe.
Werengani mutu wathunthu Numeri 24
Onani Numeri 24:9 nkhani