7 Pamene Pinehasi mwana wa Eleazara, mwana wa Aroni wansembe, anaciona, anauka pakati pa khamu, natenga nthungo m'dzanja lace;
Werengani mutu wathunthu Numeri 25
Onani Numeri 25:7 nkhani