Numeri 26:48 BL92

48 Ana amuna a Nafitali monga mwa mabanja ao ndiwo: Yazeli, ndiye kholo la banja la Ayazeli; Guni, ndiye kholo la banja la Aguni;

Werengani mutu wathunthu Numeri 26

Onani Numeri 26:48 nkhani