Numeri 26:58 BL92

58 Awa ndi mabanja a Alevi: banja la Alibini, banja la Ahebroni, banja la Amali, banja la Amusi, banja la Akohati. Ndipo Kohati anabala Amiramu.

Werengani mutu wathunthu Numeri 26

Onani Numeri 26:58 nkhani