64 Koma pakati pao panalibe mmodzi wa iwo amene anawerengedwa ndi Mose ndi Aroni wansembe, amene anawerenga ana a Israyeli m'cipululu ca Sinai.
Werengani mutu wathunthu Numeri 26
Onani Numeri 26:64 nkhani