65 Popeza Yehova adanena za iwowa, Adzafatu m'cipululu. Ndipo sanatsalira mmodzi wa iwowa koma Kalebi mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.
Werengani mutu wathunthu Numeri 26
Onani Numeri 26:65 nkhani