Numeri 30:7 BL92

7 nakazimva mwamuna wace, nakakhala naye cete tsiku lakuzimva iye; pamenepo zowinda zace zidzakhazikika, ndi zodziletsa anamanga nazo moyo wace zidzakhazikika.

Werengani mutu wathunthu Numeri 30

Onani Numeri 30:7 nkhani