28 popeza wakupha munthu akadakhala m'mudzi wace wopulumukirako kufikira atafa mkulu wa ansembe; koma atafa mkulu wa ansembe wakupha munthuyo abwere ku dziko lace lace.
Werengani mutu wathunthu Numeri 35
Onani Numeri 35:28 nkhani