Numeri 36:6 BL92

6 Colamulira Yehova za ana akazi a Tselofekadi ndi ici, kuti, Akwatibwe nao amene afuna eni ace; komatu akwatibwe nao a banja la pfuko la makolo ao okha okha.

Werengani mutu wathunthu Numeri 36

Onani Numeri 36:6 nkhani