Numeri 4:45 BL92

45 Amenewo ndiwo owerengedwa a mabanja a ana a Merari, amene Mose ndi Aroni anawawerenga monga mwa mau a Yehova mwa dzanja la Mose.

Werengani mutu wathunthu Numeri 4

Onani Numeri 4:45 nkhani