Numeri 4:46 BL92

46 Owerengedwa onse a Alevi, amene Mose ndi Aroni ndi akalonga a Israyeli anawawerengera, monga mwa mabanja ao, ndi monga mwa nyumba za makolo ao,

Werengani mutu wathunthu Numeri 4

Onani Numeri 4:46 nkhani