10 Ndipo tsiku lacisanu ndi citato adze nazo njiwa ziwiri, kapena maunda awiri, kwa wansembe, ku khomo la cihema cokomanako;
Werengani mutu wathunthu Numeri 6
Onani Numeri 6:10 nkhani