11 ndipo wansembe akonze imodzi nsembe yaucimo, ndi yina nsembe yopsereza, namtetezere popeza anacimwa nao mtembowo; ndipo apatulire mutu wace tsiku lomwelo.
Werengani mutu wathunthu Numeri 6
Onani Numeri 6:11 nkhani