Numeri 7:17 BL92

17 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, ana a nkhosa: asanu a caka cimodzi; ndico copereka ca Nahesoni mwana wa Aminadabu.

Werengani mutu wathunthu Numeri 7

Onani Numeri 7:17 nkhani