Numeri 7:47 BL92

47 ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, ana a nkhosa asanu a caka cimodzi; ndico copereka ca Eliyasafe mwana wa Deyueli.

Werengani mutu wathunthu Numeri 7

Onani Numeri 7:47 nkhani