1 Mibadwo ya ana a Nowa, Semu, Hamu, ndi Yafeti, ndi iyi; kwa iwo ndipo kunabadwa ana amuna, citapita cigumula cija.
Werengani mutu wathunthu Genesis 10
Onani Genesis 10:1 nkhani