Genesis 10:32 BL92

32 Amenewo ndi mabanja a ana a Nowa monga mwa mibadwo yao, m'mitundu yao: ndi amenewo anagawanika mitundu pa dziko lapansi, citapita cigumula.

Werengani mutu wathunthu Genesis 10

Onani Genesis 10:32 nkhani